Song of Solomon 4:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe uli ngati kasupe wothirira munda, ngati chitsime cha madzi abwino, ngati mitsinje yamadzi yochokera ku Lebanoni. Mkazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiwe kasupe wa m'minda, chitsime cha madzi amoyo, ndi mitsinje yoyenda yochokera ku Lebanoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe ndiwe kasupe wa mʼmunda, chitsime cha madzi oyenda, mtsinje wa madzi ochokera ku Lebanoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiwe kasupe wa m'minda, Citsime ca madzi amoyo, Ndi mitsinje yoyenda yocokera ku Lebano.