Song of Solomon 4:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Milomo yako ili ngati mbota yofiira, ndipo pakamwa pako mpokongola zedi. Kukhalira kumbuyo kwa nsalu yako yakumutuyo, masaya ako, akuwoneka ngati mabandu a makangaza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Milomo yako ikunga mbota yofiira, m'kamwa mwako ndi kukoma: Palitsipa pako pakunga phande la khangaza paseli pa chophimba chako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Milomo yako ili ngati mbota yofiira; pakamwa pako ndi pokongola kwambiri. Kukhalira kumbuyo kwa nsalu yako yophimba kumutuyo, masaya ako akuoneka ngati mabandu a makangadza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Milomo yako ikunga mbota yofiira, M'kamwa mwako ndi kukoma: Palitsipa pako pakunga phande la khangaza Patseri pa cophimba cako.