Song of Solomon 4:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maŵere ako ali ngati mbaŵala ziŵiri, ngati mphoyo zamapasa zimene zikudya pakati pa akakombo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mawere ako awiri akunga ana awiri a nswala obadwa limodzi, akudya pakati pa akakombo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawere ako ali ngati tiana tiwiri ta nswala, ngati ana amapasa a nswala amene akudya pakati pa maluwa okongola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maere ako awiri akunga ana awiri a nswala obadwa limodzi, Akudya pakati pa akakombo.