Song of Solomon 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene kamphepo kamadzulo kakuyamba kuuzira, ndipo mithunzi ikuthaŵa, ndidzapita mofulumira ku phiri la mure, ndi ku chitunda cha lubani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mpaka dzuwa litapepa, mithunzi ndi kutanimpha, ndikamuka kuphiri la mure, ndi kuchitunda cha lubani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kamphepo kamadzulo kakayamba kuwuzira ndipo mithunzi ikayamba kuthawa, ndidzapita ku phiri la mure ndi ku chitunda cha lubani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpaka dzuwa litapepa, mithunzi ndi kutanimpha, Ndikamuka ku phiri la nipa, Ndi ku citunda ca mtanthanyerere.