Song of Solomon 5:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wokondedwa wangayo ngwokongola, ndiponso wathanzi, wodziŵika zedi pakati pa amuna zikwi khumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wokondedwa wanga ali woyera ndi wofiira, womveka mwa zikwi khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wokondedwa wangayo ndi wowala kwambiri ndi wathanzi pakati pa anthu 1,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wokondedwa wanga ali woyera ndi wofiira, Womveka mwa zikwi khumi.