Song of Solomon 5:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso ake amaoneka okongola ngati nkhunda zitakhala pa akasupe a madzi, ngati nkhunda zitasamba mu mkaka, zitangoima bwinobwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a maso ake akunga nkhunda pambali pa mitsinje ya madzi; otsukidwa ndi mkaka, okhala pa mitsinje yodzala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso ake ali ngati nkhunda mʼmbali mwa mitsinje ya madzi, ngati nkhunda zitasamba mu mkaka, zitayima ngati miyala yamtengowapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a maso ace akunga nkhunda pambali pa mitsinje ya madzi; Otsukidwa ndi mkaka, okhala pa mitsinje yodzala.