Song of Solomon 5:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mikono yake ili ngati nthambi zagolide za makaka a miyala yamtengowapatali. Thupi lake nlosalala ngati mnyanga wanjovu woti aikamo miyala ya safiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Manja ake akunga zing'anda zagolide zoikamo zonyezimira zoti biriwiri. Thupi lake likunga chopanga cha minyanga cholemberapo masafiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manja ake ali ngati ndodo zagolide zokongoletsedwa ndi miyala yamtengowapatali. Thupi lake ndi losalala ngati mnyanga wanjovu woyikamo miyala ya safiro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Manja ace akunga zing'anda zagolidi zoikamo zonyezimira zoti biriwiri: Thupi lace likunga copanga ca minyanga colemberapo masafiro.