Song of Solomon 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zovala ndavula kale, ndingazivalenso bwanji? Ndasamba kale m'miyendo, nanga ndiidetsenso poyenda?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinayankha kuti, Ndavula malaya anga, ndiwavalenso bwanji? Ndasuka mapazi anga; ndiwadetserenji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndavula kale zovala zanga, kodi ndizivalenso? Ndasamba kale mapazi anga kodi ndiwadetsenso?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinayankha kuti, Ndabvula maraya anga, ndiwabvalenso bwanji? Ndatsuka mapazi anga; ndiwadetserenii?