Song of Solomon 5:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene wokondedwa wanga adangoti pisu dzanja pa chiboo chapachitseko, mtima wanga udachita kuti phwii!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwenzi langa analonga dzanja lake pazenera, mtima wanga ndi kuguguda chifukwa cha iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwenzi langa anapisa dzanja lake pa chibowo cha pa chitseko; mtima wanga unagunda chifukwa cha iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwenzi langa analonga dzanja lace pazenera, Mtima wanga ndi kuguguda cifukwa ca iye,