Song of Solomon 5:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu akazi a ku Yerusalemu, ndithu ndakupembani, mukampeza wokondedwa wangayo mumuuze kuti ine ndikumva chikondi chodwala nacho. Akazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikulumbirirani, ana akazi inu a ku Yerusalemu, mukapeza bwenzi langa, mudzamuuza chiyani? Kuti ndadwala ndi chikondi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu akazi a ku Yerusalemu ndithu ndikukupemphani, mukapeza wokondedwa wangayo, kodi mudzamuwuza chiyani? Muwuzeni kuti ine ndadwala nacho chikondi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikulumbirirani, ana akazi inu a ku Yerusalemu, Mukapeza bwenzi langa, mudzamuuza ciani? Kuti ndadwala ndi cikondi.