Song of Solomon 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe wokongola koposa akazi onsewe, kodi wokondedwa wakoyo ngwopambana wina aliyense bwanji? Kodi wokondedwa wakoyo ngwopambana ena onse chotani kuti uzichita kupemba motere? Mkazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwenzi lako aposa abwenzi ena bwanji, mkaziwe woposa kukongola? Bwenzi lako aposa abwenzi ena bwanji, kuti utilumbirira motero?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe wokongola kuposa akazi onsewa, kodi wokondedwa wakoyo ndi wopambana wina aliyense bwanji? Kodi wokondedwa wakoyo ndi wopambana ena onse chotani kuti uzichita kutipempha motere?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwenzi lako aposa abwenzi ena bwanji, Mkaziwe woposa kukongola? Bwenzi lako aposa abwenzi ena bwanji, Kuti utilumbirira motero?