Song of Solomon 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe wokongola koposa akazi onsewe, kodi wokondedwa wakoyo wapita kuti? Kodi wokondedwa wakoyo waloŵera potani, kuti tichite kukuthandiza kumfunafuna? Mkazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwenzi lako wapita kuti, mkaziwe woposa kukongola? Bwenzi lako wapatukira kuti, tikamfunefune pamodzi nawe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe wokongola kuposa akazi onsewa, kodi wokondedwa wakoyo wapita kuti? Kodi wokondedwa wakoyo wakhotera njira iti kuti timufunefune pamodzi ndi iwe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwenzi lako wapita kuti, Mkaziwe woposa kukongola? Bwenzi lako wapambukira kuti, Tikamfunefune pamodzi nawe?