Song of Solomon 6:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndisanazindikireko kanthu, ndidakhala ngati ndikulota kuti ndili m'galeta pambali pa mfumu yanga. Akazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndisanazindikire, moyo wanga unandiimika pakati pa magaleta a anthu anga aufulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndisanazindikire kanthu, ndinakhala ngati ndikulota kuti ndili mʼgaleta pambali pa mfumu yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndisanazindikire, moyo wanga unandiimika Pakati pa magareta a anthu anga aufulu.