Song of Solomon 6:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwerera, bwerera, iwe namwali wa ku Sulami, bwerera kuti tidzakupenyetsetse. Mkazi Chifukwa chiyani mukuti mudzandipenyetsetse ine Msulamine, pamene ndikuvina pakati pa magulu aŵiri?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anati, Bwera, bwera, Msulamiwe; bwera, bwera, tiyang'ane pa iwe. Muyang'aniranji pa Msulami, ngati pa masewero akuguba?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwerera, bwerera iwe namwali wa ku Sulami; bwerera, bwerera kuti ife tidzakupenyetsetse iwe! Chifukwa chiyani mukufuna kudzapenyetsetsa ine mwana wamkazi wa ku Sulami, pamene ndikuvina pakati pa magulu awiri?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anati, Bwera, bwera, Msulamiwe; Bwera, bwera, tiyang'ane pa iwe. Muyang'aniranji pa Msulami, Ngati pa masewero akuguba?