Song of Solomon 6:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wokondedwa wanga watsikira kumunda kwakeku, ku timinda ta mbeu zokometsera chakudya. Akukadyetsa ziŵeto zake ku minda ndiponso akukathyola akakombo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwenzi langa watsikira kumunda kwake, kuzitipula za mphoka, kukadya kumunda kwake, ndi kutchera akakombo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachikondi wanga watsikira ku munda kwake, ku timinda ta zokometsera zakudya, akukadyetsa ziweto zake ku minda, ndiponso akuthyola maluwa okongola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwenzi langa watsikira kumunda kwace, Ku zitipula za mphoka, Kukadya kumunda kwace, ndi kuchera akakombo.