Song of Solomon 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe bwenzi langa, ndiwe wokongola ngati Tiriza, wa maonekedwe abwino ngati Yerusalemu, ndiwe wochititsa mantha ngati gulu la ankhondo mbendera zili m'manja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wakongola, bwenzi langa, namwaliwe ngati Tiriza, wokoma ngati Yerusalemu, woopsa ngati nkhondo ndi mbendera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiwe wokongola, bwenzi langa, ngati Tiriza, wokongola kwambiri ngati Yerusalemu, ndiwe woopsa ngati gulu lankhondo lonyamula mbendera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakongola, bwenzi langa, namwaliwe ngati Tiriza, Wokoma ngati Yerusalemu, Woopsya ngati nkhondo ndi mbendera.