Song of Solomon 6:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kukhalira kumbuyo kwa nsalu yako yakumutuyo, masaya ako akuwoneka ngati mabandu a makangaza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palitsipa pako pakunga phande la khangaza paseli pa chophimba chako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kukhalira kumbuyo kwa nsalu yako yophimba kumutu, masaya ako ali ngati mabandu a makangadza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palitsipa pako pakunga phande la khangaza Patseri pa cophimba cako.