Song of Solomon 7:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maŵere ako akuwoneka ngati mbaŵala ziŵiri, ngati mphoyo zamapasa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mawere ako akunga ana awiri a nswala anabadwa limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawere ako akuoneka ngati ana awiri a mbawala, ngati mphoyo zamapasa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maere ako akunga ana awiri a nswala Anabadwa limodzi.