Song of Solomon 7:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukamandimpsompsona, ine kukhosi see, ngati ndikumwa vinyo wokoma kwambiri. Mkazi Tsono vinyo ameneyu amthirire wokondedwa wanga, ayenderere pa milomo yake ndi m'mano mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kamwa mwako munge ngati vinyo woposa, womeza tseketseke bwenzi langa, wolankhulitsa milomo ya ogona tulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo pakamwa pako pali ngati vinyo wokoma kwambiri. Tsono vinyo ameneyu amuthirire wachikondi wanga, ayenderere bwino pa milomo yake ndi mano ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kamwa mwako munge ngati vinyo woposa, Womeza tseketeke bwenzi langa, Wolankhulitsa milomo ya ogona tulo.