Titus 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
m'malo momasamala nthano zachiyuda, ndi malamulo a anthu okana choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osasamala nthano zachabe za Chiyuda, ndi malamulo a anthu opatuka kusiyana nacho choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti asasamalenso nthano za Chiyuda, ndi malamulo a anthu amene akukana choonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osasamala nthanu zacabe za Ciyuda, ndi malamulo a anthu opatuka kusiyana naco coonadi.