Titus 1:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi yake Mulungu, Mpulumutsi wathu, adaululadi mau ake, ndipo adalamula kuti ine ndipatsidwe udindo wolalika uthengawu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma pa nyengo za Iye yekha anaonetsa mau ake muulalikiro, umene anandisungitsa ine, monga mwa lamulo la Mpulumutsi wathu Mulungu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi yake Mulungu, Mpulumutsi wathu anawulula poyera mawu ake ndipo analamula kuti ndipatsidwe udindo wolalikira uthengawu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma pa nyengo za iye yekha anaonetsa mau ace muulalikiro, umene anandisungitsa ine, monga mwa lamulo la Mpulumutsi wathu Mulungu: