Titus 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kapena kumaŵabera, koma makamaka adziwonetse kuti ngokhulupirika pa zonse zabwino. Motero pa zochita zao zonse adzaonetsa kukoma kwake kwa zophunzitsa zonena za Mulungu, Mpulumutsi wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osatapa pa zao, komatu aonetsere chikhulupiriko chonse chabwino; kuti akakometsere chiphunzitso cha Mpulumutsi wathu Mulungu m'zinthu zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena kumawabera, koma adzionetse kuti ndi odalirika, motero pa zochita zawo zonse adzaonetsa ubwino wa chiphunzitso cha Mulungu, Mpulumutsi wathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osatapa pa zao, komatu aonetsere cikhulupiriko conse cabwino; kuti akakometsere ciphunzitso ca Mpulumutsi wathu Mulungu m'zinthu zonse.