Titus 2:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti choncho athe kuphunzitsa azimai achitsikana kukonda amuna ao ndi ana ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti akalangize akazi aang'ono akonde amuna ao, akonde ana ao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono atha kulangiza amayi achichepere kukonda amuna awo ndi ana awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti akalangize akazi ang one akonde amuna ao, akonde ana ao,