Titus 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja ukudziŵa kuti munthu wotere ngwosokonezeka ndipo ngwochimwa. Mwini wake yemwe amadziimba mlandu yekha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
podziwa kuti wotereyo wasandulika konse, nachimwa, nakhala wodzitsutsa yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe udziwe kuti munthu wotero ngosokoneza ndi wochimwa, ndipo akudzitsutsa yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
podziwa kuti worereyo wasandulika konse, nacimwa, nakhala wodzitsutsa Yekha.