Titus 3:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu athunso aziphunzira kudzipereka pa ntchito zabwino, kuti azithandiza pamene pali kusoŵa kwenikweni. Azitero kuti moyo wao usakhale wopanda phindu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu athu aphunzirenso asunge ntchito zabwino zofunika, kuti asakhale osabala zipatso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu athu aphunzire kudzipereka pogwira ntchito zabwino, nʼcholinga chakuti athandize zinthu zimene zikufunika msangamsanga. Ndipo asakhale moyo osapindulitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu athu aphunzirenso asunge nchito zabwino zofunika, kuti asakhale osabala zipstso.