Zechariah 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mngeloyo anandiwuza kuti, ‘Lengeza kuti, Chauta Wamphamvuzonse akuti, “Maganizo anga onse ndi mtima wanga wonse zili pa Yerusalemu ndi Ziyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mthenga wakulankhula ndi ine anati kwa ine, fuula, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Ndichitira nsanje Yerusalemu ndi Ziyoni ndi nsanje yaikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mngelo amene ankayankhula nane anati, “Lengeza mawu awa: Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Ine ndikuchitira nsanje Yerusalemu ndi Ziyoni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mthenga wakulankhula ndi ine anati kwa ine, Pfuula, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Ndicitira nsanje Yerusalemu ndi Ziyoni ndi nsanje yaikuru.