Zechariah 1:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi makolo anuwo ali kuti tsopano? Nanga aneneri, kodi amakhalapo mpaka muyaya?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Makolo anu, ali kuti iwowo? Ndi aneneri, akhala ndi moyo kosatha kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi makolo anuwo ali kuti tsopano? Nanga aneneri, kodi amakhalapo mpaka muyaya?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Makolo anu, ali kut iwowo? ndi alieneri, akhala nd moyo kosatha kodi?