Zechariah 1:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku la 24 la mwezi wa khumi ndi umodzi, mwezi wa Sebati, chaka chachiŵiri cha ufumu wa Dariusi, Chauta adapatsa uthenga mneneri Zekariya, mwana wa Berekiya, mdzukulu wa Ido. Tsono Zekariya adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku la makumi awiri ndi chinai la mwezi wakhumi ndi chimodzi, ndiwo mwezi wa Sebati, chaka chachiwiri cha Dariusi, mau a Yehova anadza kwa Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido mneneri, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku la 24 la mwezi wa 11, mwezi wa Sebati, chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo, Yehova anayankhula ndi Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku la makumi awiri ndi cinai la mwezi wakhumi ndi cimodzi, ndiwo mwezi wa Segati, caka caciwiri ca Dariyo, mau a Yehova anadza kwa Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido mneneri, ndi kuti,