Zechariah 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ayuda onse pamodzi adzakhala ngati ngwazi zankhondo, zopondereza adani m'matope am'miseu nthaŵi yankhondo. Adzamenya nkhondo chifukwa choti Chauta ali nawo, ndipo adzagonjetsa adani okwera pa akavalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzakhala ngati ngwazi zakupondereza adani m'thope la kubwalo kunkhondo; ndipo adzachita nkhondo, chifukwa Yehova ali nao; ndi apakavalo adzachitidwa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse pamodzi adzakhala ngati ngwazi zankhondo zoponda mʼmatope a mʼmisewu nthawi yankhondo. Chifukwa Yehova adzakhala nawo, adzachita nkhondo ndi kugonjetsa okwera pa akavalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzakhala ngati ngwazi zakupondereza adani m'thope la kubwalo kunkhondo; ndipo adzacita nkhondo, cifukwa Yehova ali nao; ndi apakavalo adzacitidwa manyazi.