Zechariah 10:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndidaŵabalalitsira pakati pa mitundu ya anthu, komabe ku maiko akutaliwo adzandikumbukira. Iwowo pamodzi ndi ana ao adzakhala moyo nadzabwerera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzawafesa mwa mitundu ya anthu, ndipo adzandikumbukira m'maiko akutali; nadzakhala pamodzi ndi ana ao, nadzabwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinawamwaza pakati pa mitundu ina ya anthu, koma ku mayiko akutaliwo adzandikumbukira. Iwo pamodzi ndi ana awo adzapulumuka, ndipo adzabwerera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzawafesa mwa mitundu ya anthu, ndipo adzandikumbukila m'maiko akutali; nadzakhala pamodzi ndi ana ao, nadzabwera.