Zechariah 12:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Banja la Levi lidzalira palokha, akazi akenso adzalira paokha. Banja la Simei lidzalira palokha, akazi akenso adzalira paokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nyumba ya Levi pamodzi ndi akazi awo, fuko la Simei pamodzi ndi akazi awo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;