Zechariah 12:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo atsogoleri a Yuda adzavomera kuti, ‘Indedi, anthu a ku Yerusalemu amapeza mphamvu mwa Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wao.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akalonga a Yuda adzanena m'mtima mwao, Okhala m'Yerusalemu ndiwo mphamvu yanga m'Yehova wa makamu Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo atsogoleri a Yuda adzayankhula mʼmitima mwawo kuti, ‘Anthu a ku Yerusalemu ndi amphamvu, chifukwa Yehova Wamphamvuzonse ndiye Mulungu wawo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akalonga a Yuda adzanena m'mtima mwao, Okhala m'Yerusalemu ndiwo mphamvu yanga m'Yehova wa makamu Mulungu wao.