Zechariah 12:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chauta adzayamba wapulumutsa mahema onse a ku Yuda, kuti ulemerero wonse wa banja la Davide ndi wa anthu a ku Yerusalemu usapambane ulemerero wa Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova adzayamba kupulumutsa mahema a Yuda, kuti ulemerero wa nyumba ya Davide ndi ulemerero wa okhala m'Yerusalemu usakulire Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova adzapulumutsa malo okhala Yuda poyamba, kuti ulemu wa nyumba ya Davide ndi wa anthu okhala mu Yerusalemu usapambane ulemu wa Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova adzayamba kupulumutsa mahema a Yuda, kuti ulemerero wa nyumba ya Davide ndi ulemerero wa okhala m'Yerusalemu usakulire Yuda.