Zechariah 14:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adzakhala mfumu ya dziko lonse lapansi. Tsiku limenelo Chauta yekha anthu onse adzampembedza, adzamdziŵa ndi dzina lake limodzi lokhalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova adzakhala mfumu ya dziko lonse; tsiku lomwelo Yehova adzakhala Iye yekha, ndi dzina lake ilo lokha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova adzakhala mfumu pa dziko lonse lapansi. Tsiku limenelo padzakhala Ambuye mmodzi yekha, ndipo dzina lidzakhala limodzi lomwelo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova adzakhala mfumu ya dziko lonse; tsiku lomwelo Yehova adzakhala Iye yekha, ndi dzina lace ilo lokha.