Zechariah 2:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Woyamba uja adauza mnzakeyo kuti, “Thamangira mnyamata wachingweyo, ukamuuze kuti mu Yerusalemu mudzakhala anthu ambiri ndiponso zoŵeta zochuluka, kotero kuti mzindawo udzakhala wopanda malinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena naye, Thamanga, lankhula ndi mnyamata uyu, ndi kuti, M'Yerusalemu mudzakhala anthu ngati m'midzi yopanda malinga, chifukwa cha kuchuluka anthu ndi zoweta momwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anamuwuza kuti, “Thamanga, kamuwuze mnyamatayo kuti, ‘Yerusalemu udzakhala mzinda wopanda malinga chifukwa mudzakhala anthu ambiri ndiponso ziweto zochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena naye, Thamanga, lankhula ndi mnyamata uyu, ndi kuti, M'Yerusalemu mudzakhala anthu ngati m'midzi yopanda malinga, cifukwa ca kucuruka anthu ndi zoweta momwemo.