Zechariah 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mngelo wa Chauta uja adauza Yoswa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mthenga wa Yehova anamchitira Yoswa umboni, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Yehova analimbikitsa Yoswa kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mthenga wa Yehova anamcitira Yoswa umboni, ndi kuti,