Zechariah 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Akupita nalo ku dziko la Sinara kuti akalimangire nyumba. Nyumbayo ikadzatha, adzakhazikamo gondololo pa phaka lake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Kummangira nyumba m'dziko la Sinara; kuti amuike efayo, namkhazikeko pa malo kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Ku dziko la Babuloni kuti akalimangire nyumba. Nyumbayo ikadzatha, adzayikamo dengulo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Kummangira nyumba m'dziko la Sinara; kuti amuike, namkhazikeko pa kuzika kwace.