Zechariah 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye amene adzamange Nyumba ya Chauta. Ndiye amene adzakhale ndi ukulu waufumu, ndi kumalamulira atakhala pa mpando wake waufumu. Pafupi ndi mpando wake padzakhala wansembe, ndipo aŵiriwo adzagwira ntchito mwamtendere ndi mogwirizana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
inde adzamanga Kachisi wa Yehova; nadzasenza ulemererowo, nadzakhala ndi kulamulira pa mpando wachifumu wake; nadzakhala wansembe pampando wachifumu wake; ndi uphungu wa mtendere udzakhala pakati pa iwo awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye amene adzamange Nyumba ya Yehova, adzalandira ulemerero waufumu ndipo adzalamulira pa mpando wake waufumu. Adzakhalanso wansembe pa mpando wake waufumu. Ndipo padzakhala mtendere.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
inde adzamanga Kacisi wa Yehova; nadzasenza ulemererowo, nadzakhala ndi kulamulira pa mpando wacifumu wace; nadzakhala wansembe pampando wacifumu wace; ndi uphungu wa mtendere udzakhala pakati pa iwo awiri,