Zechariah 6:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chisoti chaufumucho azidzachisunga m'Nyumba ya Chauta, kuti chikhale chikumbutso kwa Heledai, Tobiya, Yedaya ndi Yosiya, mwana wa Zefaniya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akorona adzakhala wa Helidai, ndi wa Tobiya, ndi wa Yedaya, ndi wa Heni mwana wa Zefaniya, akhale chikumbutso m'Kachisi wa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chipewa cha ufumucho adzachipereka kwa Helemu, Tobiya, Yedaya, ndi kwa Heni mwana wa Zefaniya, kuti chikhale chikumbutso mʼNyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akorona adzakhala wa Kelemu, ndi wa Tobiya, ndi wa Yedaya, ndi wa Keni mwana wa Zefaniya, akhale cikumbutso m'Kacisi wa Yehova.