Zechariah 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Galeta loyamba linkakokedwa ndi akavalo ofiira, lachiŵiri akavalo akuda,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ku galeta woyamba kunali akavalo ofiira; ndi kugaleta wachiwiri akavalo akuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Galeta loyamba limakokedwa ndi akavalo ofiira, lachiwiri ndi akavalo akuda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ku gareta woyamba kunali akavalo ofiira; ndi ku gareta waciwiri akavalo akuda;