Zechariah 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
lachitatu akavalo oyera, lachinai linkakokedwa ndi akavalo otuŵa a maŵanga ofiirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kugaleta wachitatu a kavalo oyera; ndi kugaleta wachinai akavalo olimba amawanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
lachitatu ndi akavalo oyera, ndipo lachinayi ndi akavalo otuwa a mawanga ofiirira, onsewa anali akavalo amphamvu kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ku gareta wacitatu akavalo oyera; ndi ku gareta wacinai akavalo olimba amawanga.