Zechariah 6:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidafunsa mngelo amene ndinkalankhula naye uja kuti, “Mbuye wanga, kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinayankha ndinati kwa mthenga wolankhula ndi ine, Izi nziyani, mbuyanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinafunsa mngelo amene amayankhula nane uja kuti, “Kodi mbuye wanga chimenechi nʼchiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinayankha ndinati kwa mthenga wolankhula ndi ine, Izi nziani, mbuyanga?