Zechariah 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mngeloyo adandiŵuza mokweza mau kuti, “Amene apita ku dziko lakumpotowo atsitsa mzimu wanga kumeneko.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anandiitana, nanena nane, kuti, Taonani, iwo akutuluka kunka kudziko la kumpoto anapumulitsa Mzimu wanga m'dziko la kumpoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anandiyitana, “Taona, akavalo amene apita ku dziko la kumpoto apumulitsa Mzimu wanga kumeneko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anandiitana, nanena nane, kuti, Taonani, iwo akuturuka kumka ku dziko la kumpoto anapumulitsa Mzimu wanga m'dziko lakumpoto.