Zechariah 7:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chachinai cha ufumu wa Dariusi, tsiku lachinai la Kisilevi, mwezi wachisanu ndi chinai, Chauta adapatsa Zekariya uthenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunachitika chaka chachinai cha mfumu Dariusi, mau a Yehova anadza kwa Zekariya tsiku lachinai la mwezi wachisanu ndi chinai, ndiwo Kisilevi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chaka chachinayi cha Mfumu Dariyo, pa tsiku lachinayi la Kisilevi, mwezi wachisanu ndi chinayi, Yehova anayankhula ndi Zekariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunacitika caka cacinai ca mfumu Dariyo, mau a Yehova anadza kwa Zekariya tsiku lacinai la mwezi wacisanu ndi cinai, ndiwo Kisilevi.