Zechariah 7:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Betele anali atatuma Sarezere ndi Regemumeleki ndi anthu ao, kuti akapemphe chifundo kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo a ku Betele anatuma Sarezere ndi Regemumeleke ndi anthu ao, apepeze Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Beteli anali atatuma Sarezeri ndi Regemu-Meleki pamodzi ndi anthu awo, kuti akapemphe chifundo kwa Yehova
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo a ku Beteli anatuma Sarezere ndi Regemeleke ndi anthu ao, apepeze Yehova,