Zechariah 7:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwinanso adaati akafunse ansembe a ku Nyumba ya Chauta Wamphamvuzonse ndiponso aneneri kuti, “Kodi ifeyo tizilira ndi kusala chakudya pa mwezi wachisanu monga m'mene takhala tikuchitira pa zaka zambiri?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wachisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikachitira zaka izi zambiri?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pokafunsa kwa ansembe a ku Nyumba ya Yehova Wamphamvuzonse ndi aneneri kuti, “Kodi ine ndizilira ndi kusala zakudya pa mwezi wachisanu, monga mmene ndakhala ndikuchitira pa zaka zambiri?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wacisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikacitira zaka izi zambiri?