Zechariah 7:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi pamene munkadya ndi kumwa, suja munkangodzikondweretsa nokha?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene mukadya si ndinu, mukamwa si ndinu kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pamene munkadya ndi kumwa, kodi simunkachita zimenezi podzisangalatsa nokha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene mukadya, ndi pamene mukamwa, mukadya si ndinu, mukamwa si ndinu kodi?