Zechariah 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma masiku ano ndatsimikiza kuti ndimchitira zabwino Yerusalemu ndi banja la Yuda. Choncho musaope.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
momwemonso ndinalingirira masiku ano kuchitira chokoma Yerusalemu ndi nyumba ya Yuda; musaopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho tsopano ndatsimikiza mtima kuchitiranso zabwino Yerusalemu ndi Yuda. Musachite mantha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
momwemonso ndinalingirira masiku ano kucitira cokoma Yerusalemu ndi nyumba ya Yuda; musaopa.