Zechariah 8:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Chauta Wamphamvuzonse ndi izi: Anthu a mitundu yambiri ndi anthu okhala m'mizinda yambiri adzabweradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova wa makamu: Kudzachitikanso kuti mitundu ya anthu, ndi okhalamo m'midzi yambiri adzafika,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Anthu a mitundu yambiri ndi anthu okhala mʼmizinda yambiri adzabwerabe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova wa makamu: Kudzacitikanso kuti mitundu ya anthu, ndi okhalamo m'midzi yambiri adzafika,