Zechariah 8:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mzinda wina adzapita ku mzinda wina, kukanena kuti, ‘Tiyeni mwamsanga tikapemphe chifundo kwa Chauta, tikapembedze Chauta Wamphamvuzonse. Ifeyo tikupita komweko.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi okhala m'mudzi umodzi adzamuka kumudzi wina, ndi kuti, Tiyeni msanga kukapepeza Yehova, ndi kufunafuna Yehova wa makamu; ndimuka inenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo nzika za mzinda wina zidzapita ku mzinda wina, kukanena kuti, ‘Tiyeni mwamsanga tikapemphe madalitso kwa Yehova ndi kukapembedza Yehova Wamphamvuzonse. Inenso ndikupita kumeneko.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi okhala m'mudzi umodzi adzamuka ku mudzi wina, ndi kuti, Tiyeni msanga kukapepeza Yehova, ndi kufunafuna Yehova wa makamu; ndimuka inenso.